Salimo 119:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndimadzuka pakati pa usiku kuti ndikuyamikeni+Chifukwa cha zigamulo zanu zolungama.