Salimo 119:116 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 116 Inu Mulungu, ndithandizeni mogwirizana ndi zimene munalonjeza,*+Kuti ndikhalebe ndi moyo.Musalole kuti ndichite manyazi chifukwa cha chiyembekezo changa.*+
116 Inu Mulungu, ndithandizeni mogwirizana ndi zimene munalonjeza,*+Kuti ndikhalebe ndi moyo.Musalole kuti ndichite manyazi chifukwa cha chiyembekezo changa.*+