Salimo 119:153 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 153 Onani mavuto anga ndipo mundipulumutse,+Chifukwa sindinaiwale chilamulo chanu.