Salimo 119:154 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 154 Nditetezeni pa mlandu wanga* ndipo mundipulumutse.+Ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo mogwirizana ndi lonjezo lanu.*
154 Nditetezeni pa mlandu wanga* ndipo mundipulumutse.+Ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo mogwirizana ndi lonjezo lanu.*