Salimo 119:162 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 162 Ndimasangalala ndi mawu anu,+Mofanana ndi munthu amene wapeza chuma chambiri.