Salimo 119:171 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 171 Milomo yanga isefukire ndi mawu okutamandani,+Chifukwa mumandiphunzitsa malamulo anu.