Salimo 119:176 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 176 Ndasochera ngati nkhosa yotayika.+ Ndifunefuneni ine mtumiki wanu,Chifukwa sindinaiwale malamulo anu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:176 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, tsa. 20
176 Ndasochera ngati nkhosa yotayika.+ Ndifunefuneni ine mtumiki wanu,Chifukwa sindinaiwale malamulo anu.+