Salimo 122:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pemphererani mtendere wa Yerusalemu.+ Amene amakukonda, mzinda iwe, adzakhala otetezeka.