-
Salimo 122:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mtendere upitirize kukhala mʼmalo ako otchingidwa ndi mpanda wolimba,
Chitetezo chipitirize kukhala munsanja zako zokhala ndi mpanda wolimba.
-