Salimo 125:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma anthu amene apatuka panjira yabwino nʼkuyamba kuyenda mʼnjira zokhotakhota,Yehova adzawachotsa limodzi ndi anthu ochita zoipa.+ Mu Isiraeli mukhale mtendere.
5 Koma anthu amene apatuka panjira yabwino nʼkuyamba kuyenda mʼnjira zokhotakhota,Yehova adzawachotsa limodzi ndi anthu ochita zoipa.+ Mu Isiraeli mukhale mtendere.