Salimo 127:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wosangalala ndi mwamuna amene wadzaza kachikwama kake ka mivi ndi mivi imeneyo.+ Abambo oterowo sadzachita manyazi,Chifukwa ana awo adzalankhula ndi adani pageti la mzinda. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 127:5 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, ptsa. 13-16
5 Wosangalala ndi mwamuna amene wadzaza kachikwama kake ka mivi ndi mivi imeneyo.+ Abambo oterowo sadzachita manyazi,Chifukwa ana awo adzalankhula ndi adani pageti la mzinda.