Salimo 130:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa inu mumakhululuka ndi mtima wonse,+Kuti anthu azikuopani.+