Salimo 130:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Isiraeli apitirize kuyembekezera Yehova,Chifukwa Yehova amasonyeza chikondi chokhulupirika,+Ndipo ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu.
7 Isiraeli apitirize kuyembekezera Yehova,Chifukwa Yehova amasonyeza chikondi chokhulupirika,+Ndipo ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu.