Salimo 135:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamandani Ya, chifukwa Yehova ndi wabwino.+ Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, chifukwa kuchita zimenezi nʼkosangalatsa.
3 Tamandani Ya, chifukwa Yehova ndi wabwino.+ Muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake, chifukwa kuchita zimenezi nʼkosangalatsa.