Salimo 135:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amachititsa kuti mitambo* ikwere kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima.Amatulutsa mphepo kuchokera mʼnyumba zake zosungira zinthu.+
7 Amachititsa kuti mitambo* ikwere kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima.Amatulutsa mphepo kuchokera mʼnyumba zake zosungira zinthu.+