Salimo 135:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anapha Sihoni mfumu ya Aamori,+Ogi mfumu ya Basana+Komanso anawononga maufumu onse a ku Kanani.