Salimo 137:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lilime langa limamatire mʼkamwa mwangaNgati sindingakukumbukire,Ngati sindingaike Yerusalemu pamwambaPa chilichonse chimene chimandisangalatsa kwambiri.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 137:6 Nsanja ya Olonda,10/15/1998, ptsa. 13-14 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 141-142, 147
6 Lilime langa limamatire mʼkamwa mwangaNgati sindingakukumbukire,Ngati sindingaike Yerusalemu pamwambaPa chilichonse chimene chimandisangalatsa kwambiri.+