Salimo 137:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, kumbukiraniZimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa. Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 137:7 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 124, 147-148
7 Inu Yehova, kumbukiraniZimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa. Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+