Salimo 138:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale nditakumana ndi mavuto, inu mudzandithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.+ Mumagwiritsa ntchito mphamvu zanu polimbana ndi adani anga omwe ndi okwiya.Dzanja lanu lamanja lidzandipulumutsa.
7 Ngakhale nditakumana ndi mavuto, inu mudzandithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.+ Mumagwiritsa ntchito mphamvu zanu polimbana ndi adani anga omwe ndi okwiya.Dzanja lanu lamanja lidzandipulumutsa.