Salimo 139:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale mdimawo sudzakhala mdima wandiweyani kwa inu,Koma usiku udzawala ngati masana.+Mdima udzangokhala ngati kuwala kwa inu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 139:12 Nsanja ya Olonda,10/1/1993, ptsa. 12-141/15/1990, ptsa. 22-23
12 Ngakhale mdimawo sudzakhala mdima wandiweyani kwa inu,Koma usiku udzawala ngati masana.+Mdima udzangokhala ngati kuwala kwa inu.+