Salimo 139:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho kwa ine maganizo anu ndi ofunika kwambiri, inu Mulungu,+ Ndipo ndi ochuluka kwambiri.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 139:17 Nsanja ya Olonda,6/15/2007, tsa. 2310/1/1993, ptsa. 16-181/15/1990, tsa. 23