Salimo 139:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu,+Ndipo ndimanyansidwa ndi anthu amene amakupandukirani.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 139:21 Galamukani!,12/8/1997, tsa. 14 Nsanja ya Olonda,10/1/1993, tsa. 191/15/1990, tsa. 24
21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu,+Ndipo ndimanyansidwa ndi anthu amene amakupandukirani.+