Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 141:5 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 57 Nsanja ya Olonda,4/15/2015, tsa. 31
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.