Salimo 141:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mafupa athu amwazika pakamwa pa Manda,*Mofanana ndi dothi limene limamwazika munthu akamalima.