-
Salimo 143:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mdani akundifunafuna.
Iye wandipondereza ndipo wandigonjetsa.
Wandichititsa kuti ndikhale mumdima ngati anthu amene anafa kalekale.
-