Salimo 143:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikukumbukira masiku akale.Ndimaganizira mozama zochita zanu zonse.+Ndimaganizira* ntchito ya manja anu ndi mtima wonse. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 143:5 Nsanja ya Olonda,12/15/1996, ptsa. 11-12
5 Ndikukumbukira masiku akale.Ndimaganizira mozama zochita zanu zonse.+Ndimaganizira* ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.