Salimo 143:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.Ndikuyembekezera inu ngati dziko louma limene likuyembekezera kuti mvula igwe.+ (Selah) Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 143:6 Nsanja ya Olonda,12/15/1996, tsa. 13
6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.Ndikuyembekezera inu ngati dziko louma limene likuyembekezera kuti mvula igwe.+ (Selah)