Salimo 143:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo chifukwa cha dzina lanu. Ndipulumutseni mʼmavuto anga, chifukwa ndinu wachilungamo.+
11 Inu Yehova, ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo chifukwa cha dzina lanu. Ndipulumutseni mʼmavuto anga, chifukwa ndinu wachilungamo.+