Salimo 144:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, tsitsani* kumwamba ndipo mutsike.+Khudzani mapiri ndipo muwachititse kuti afuke utsi.+