-
Salimo 144:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mukatero ana athu aamuna adzakhala ngati mitengo ingʼonoingʼono imene ikukula mofulumira,
Ndipo ana athu aakazi adzakhala ngati zipilala zamʼmakona zosemedwa mwaluso, kuti akazigwiritse ntchito pomanga nyumba yachifumu.
-