-
Salimo 144:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nyumba zathu zosungiramo zinthu zizadzaza ndi zokolola zamitundu yosiyanasiyana.
Nkhosa zathu zidzaswana nʼkukhala masauzandemasauzande kapena masauzande ambirimbiri.
-