-
Salimo 144:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ngʼombe zathu zimene zili ndi bere, sizidzavulala kapena kubereka ana akufa.
Ndipo mʼmabwalo athu simudzamveka kulira kwa munthu amene ali pamavuto.
-