Salimo 146:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mpweya* wake umachoka, ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene amaganiza zimatheratu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 146:4 Nsanja ya Olonda,4/1/1999, ptsa. 16-17 Kukambitsirana, ptsa. 191, 298, 322
4 Mpweya* wake umachoka, ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene amaganiza zimatheratu.+