Salimo 146:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amene amaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa anthu amene achitiridwa chinyengo,Amene amapereka chakudya kwa anthu anjala.+ Yehova akumasula anthu amene ali mʼndende.*+
7 Amene amaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa anthu amene achitiridwa chinyengo,Amene amapereka chakudya kwa anthu anjala.+ Yehova akumasula anthu amene ali mʼndende.*+