Salimo 147:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amatumiza mawu ake ndipo matalalawo amasungunuka. Amachititsa mphepo yake kuwomba,+ ndipo madzi amayenda. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 147:18 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2017, tsa. 20
18 Amatumiza mawu ake ndipo matalalawo amasungunuka. Amachititsa mphepo yake kuwomba,+ ndipo madzi amayenda.