Salimo 148:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye adzawonjezera mphamvu* za anthu ake,Kuti anthu ake onse okhulupirika atamandike,Amene ndi ana a Isiraeli, anthu amene ali pafupi ndi iye. Tamandani Ya!*
14 Iye adzawonjezera mphamvu* za anthu ake,Kuti anthu ake onse okhulupirika atamandike,Amene ndi ana a Isiraeli, anthu amene ali pafupi ndi iye. Tamandani Ya!*