Salimo 150:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mutamandeni poliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+ Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe komanso zeze.+
3 Mutamandeni poliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+ Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe komanso zeze.+