Miyambo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yothandiza munthu wosadziwa zinthu kuti akhale wozindikira.+Yothandiza wachinyamata kuti akhale wodziwa zinthu komanso kuti aziganiza bwino.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda,12/15/2002, tsa. 309/15/1999, ptsa. 12-13
4 Yothandiza munthu wosadziwa zinthu kuti akhale wozindikira.+Yothandiza wachinyamata kuti akhale wodziwa zinthu komanso kuti aziganiza bwino.+