Miyambo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Izi ndi zimene anthu ofuna kupeza phindu mwachinyengo amachita,Ndipo phindu limene apezalo lidzachotsa moyo wawo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,9/15/1999, tsa. 15
19 Izi ndi zimene anthu ofuna kupeza phindu mwachinyengo amachita,Ndipo phindu limene apezalo lidzachotsa moyo wawo.+