Miyambo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ikufuula pamphambano ya* misewu yodutsa anthu ambiri. Pamageti olowera mumzinda, ikunena kuti:+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:21 Nsanja ya Olonda,9/15/1999, tsa. 15