Miyambo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa ine ndinaitana, koma inu munapitiriza kukana,Ndinatambasula dzanja langa, koma palibe amene anafuna kuti ndimuthandize.+
24 Chifukwa ine ndinaitana, koma inu munapitiriza kukana,Ndinatambasula dzanja langa, koma palibe amene anafuna kuti ndimuthandize.+