Miyambo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wosangalala ndi munthu amene amapeza nzeru,+Ndiponso munthu amene amaphunzira zinthu zimene zingamuthandize kukhala wozindikira. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Nsanja ya Olonda,12/15/1993, tsa. 19
13 Wosangalala ndi munthu amene amapeza nzeru,+Ndiponso munthu amene amaphunzira zinthu zimene zingamuthandize kukhala wozindikira. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Nsanja ya Olonda,12/15/1993, tsa. 19