Miyambo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuyenda mʼnjira zake kumasangalatsa,Ndipo kuyenda mʼmisewu yake kumabweretsa mtendere.+