Miyambo 3:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Onyoza, iye amawanyoza,+Koma ofatsa amawakomera mtima.+