Miyambo 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anzeru adzalandira ulemu,Koma opusa amalemekeza zinthu zimene zidzawachititse manyazi.+