Miyambo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Upeze nzeru, upezenso luso lomvetsa zinthu.+ Usaiwale ndipo usapatuke pa zimene ndimakuuza. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:5 Nsanja ya Olonda,5/15/2000, ptsa. 20-21