Miyambo 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Salaza* njira imene phazi lako likuyenda,+Ndipo njira zako zonse zidzakhala zotetezeka.