Miyambo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanga, uzitsatira malamulo a bambo ako,Ndipo usasiye kutsatira malangizo* a mayi ako.+