Miyambo 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aliyense wochita chigololo ndi mkazi ndi wopanda nzeru.*Amene amachita zimenezi amadzibweretsera mavuto aakulu pa moyo wake.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:32 Nsanja ya Olonda,9/15/2000, tsa. 28 Kukambitsirana, tsa. 171
32 Aliyense wochita chigololo ndi mkazi ndi wopanda nzeru.*Amene amachita zimenezi amadzibweretsera mavuto aakulu pa moyo wake.+