Miyambo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa cha ine, mafumu amalamulira,Ndipo akuluakulu a boma amakhazikitsa malamulo olungama.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:15 Nsanja ya Olonda,3/15/2001, tsa. 27